Yobu 33:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Iye wandiwombola kuti ndisapite kudzenje,+Ndipo moyo wanga udzaona kuwala.’ Salimo 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti simudzasiya moyo wanga m’Manda.+Simudzalola kuti wokhulupirika wanu aone dzenje.+ Salimo 30:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu Yehova, mwanditulutsa m’Manda,+Mwandisunga ndi moyo, kuti ndisatsikire m’dzenje.+ Salimo 56:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti inu mwalanditsa moyo wanga ku imfa.+Inu mwateteza phazi langa kuti lisapunthwe,+Kuti ndiyendeyende pamaso pa Mulungu m’kuwala kumene kumaunikira anthu amoyo.+ Salimo 86:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti kukoma mtima kosatha kumene mwandisonyeza ndi kwakukulu,+Ndipo mwapulumutsa moyo wanga ku Manda, kumalo apansi penipeni.+
13 Pakuti inu mwalanditsa moyo wanga ku imfa.+Inu mwateteza phazi langa kuti lisapunthwe,+Kuti ndiyendeyende pamaso pa Mulungu m’kuwala kumene kumaunikira anthu amoyo.+
13 Pakuti kukoma mtima kosatha kumene mwandisonyeza ndi kwakukulu,+Ndipo mwapulumutsa moyo wanga ku Manda, kumalo apansi penipeni.+