Salimo 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Imvani dandaulo lolungama, inu Yehova. Mvetserani kulira kwanga kochonderera.+Tcherani khutu ku pemphero langa limene likutuluka pamilomo yopanda chinyengo.+ Salimo 55:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Inu Mulungu, mvetserani pemphero langa.+Musanyalanyaze pempho langa lakuti mundikomere mtima.+ Afilipi 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Musamade nkhawa ndi kanthu kalikonse,+ koma pa chilichonse, mwa pemphero ndi pembedzero,+ pamodzi ndi chiyamiko, zopempha zanu zidziwike kwa Mulungu.+
17 Imvani dandaulo lolungama, inu Yehova. Mvetserani kulira kwanga kochonderera.+Tcherani khutu ku pemphero langa limene likutuluka pamilomo yopanda chinyengo.+
6 Musamade nkhawa ndi kanthu kalikonse,+ koma pa chilichonse, mwa pemphero ndi pembedzero,+ pamodzi ndi chiyamiko, zopempha zanu zidziwike kwa Mulungu.+