Salimo 110:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 110 Yehova wauza Ambuye wanga kuti:+“Khala kudzanja langa lamanja+Kufikira nditaika adani ako monga chopondapo mapazi ako.”+ Machitidwe 2:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndipotu Davide sanakwere kumwamba,+ koma iye mwini anati, ‘Yehova anauza Ambuye wanga kuti: “Khala kudzanja langa lamanja+ 1 Akorinto 15:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pakuti ayenera kulamulira monga mfumu kufikira Mulungu ataika adani onse pansi pa mapazi+ ake. Aheberi 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma kodi ndi mngelo uti amene anamuuzapo kuti: “Khala kudzanja langa lamanja, kufikira nditaika adani ako monga chopondapo mapazi ako”?+ Aheberi 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kuyambira pamenepo, akuyembekezera kufikira pamene adani ake adzaikidwe monga chopondapo mapazi ake.+
110 Yehova wauza Ambuye wanga kuti:+“Khala kudzanja langa lamanja+Kufikira nditaika adani ako monga chopondapo mapazi ako.”+
34 Ndipotu Davide sanakwere kumwamba,+ koma iye mwini anati, ‘Yehova anauza Ambuye wanga kuti: “Khala kudzanja langa lamanja+
13 Koma kodi ndi mngelo uti amene anamuuzapo kuti: “Khala kudzanja langa lamanja, kufikira nditaika adani ako monga chopondapo mapazi ako”?+
13 Kuyambira pamenepo, akuyembekezera kufikira pamene adani ake adzaikidwe monga chopondapo mapazi ake.+