12 Pakuti pa nthawi ino sitikuona bwinobwino chifukwa tikugwiritsa ntchito galasi losaoneka bwinobwino,+ koma pa nthawiyo zidzakhala maso ndi maso.+ Pa nthawi ino zimene ndikudziwa n’zoperewera, koma pa nthawiyo ndidzadziwa bwinobwino ngati mmene ineyo ndikudziwikira bwinobwino.+
6 Pakuti Mulungu ndiye anati: “Kuwala kuunike kuchokera mu mdima,”+ ndipo kudzera mwa nkhope ya Khristu,+ waunika mitima yathu kuti iwale+ ndi ulemerero wokhudzana ndi kudziwa+ Mulungu.