Miyambo 22:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Tchera khutu lako ndi kumva mawu a anthu anzeru,+ kuti ulandire ndi mtima wonse nzeru zochokera kwa ine.+ Machitidwe 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano ataona mmene Petulo ndi Yohane anali kulankhulira molimba mtima, komanso atazindikira kuti anali anthu osaphunzira ndiponso anthu wamba,+ anadabwa kwambiri. Ndipo anayamba kuwazindikira kuti anali kuyenda ndi Yesu.+ Aheberi 10:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndipo tiyeni tiganizirane kuti tilimbikitsane+ pa chikondi ndi ntchito zabwino.+
17 Tchera khutu lako ndi kumva mawu a anthu anzeru,+ kuti ulandire ndi mtima wonse nzeru zochokera kwa ine.+
13 Tsopano ataona mmene Petulo ndi Yohane anali kulankhulira molimba mtima, komanso atazindikira kuti anali anthu osaphunzira ndiponso anthu wamba,+ anadabwa kwambiri. Ndipo anayamba kuwazindikira kuti anali kuyenda ndi Yesu.+