Levitiko 26:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 pamenepo ndidzatsutsana nanu koopsa,+ ndipo ineyo ndidzakukwapulani maulendo 7 chifukwa cha machimo anu.+ Deuteronomo 32:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndidzawonjezera masoka awo,+Mivi yanga ndidzaithera pa iwo.+ Yeremiya 4:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Alengeza za kuphwanya kosakaziratu pakuti dziko lonse lafunkhidwa.+ Mwadzidzidzi, mahema anga ndi nsalu za mahema angawo zafunkhidwa+ m’kanthawi kochepa.
28 pamenepo ndidzatsutsana nanu koopsa,+ ndipo ineyo ndidzakukwapulani maulendo 7 chifukwa cha machimo anu.+
20 Alengeza za kuphwanya kosakaziratu pakuti dziko lonse lafunkhidwa.+ Mwadzidzidzi, mahema anga ndi nsalu za mahema angawo zafunkhidwa+ m’kanthawi kochepa.