Numeri 13:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Atafika kuchigwa* cha Esikolo,+ anadula nthambi yokhala ndi tsango limodzi la mphesa,+ ndipo anthu awiri analinyamula paphewa ndi mitengo yonyamulira. Anatengakonso makangaza*+ ndi nkhuyu. Yesaya 28:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Nkhata yamaluwa yokongola imene maluwa ake akufota,+ yomwe ili pamwamba pa phiri m’chigwa chachonde, idzakhala ngati nkhuyu yoyambirira kucha+ chilimwe chisanafike, imene munthu akaiona amaithyola n’kuimeza msangamsanga. Mika 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tsoka kwa ine,+ chifukwa ndakhala ngati munthu wanjala amene sanapeze zipatso kuti adye.+ Ndakhala ngati munthu amene sanapeze nkhuyu zoyambirira zimene anali kuzilakalaka, nthawi yokolola zipatso za m’chilimwe* ndi mphesa itatha.+
23 Atafika kuchigwa* cha Esikolo,+ anadula nthambi yokhala ndi tsango limodzi la mphesa,+ ndipo anthu awiri analinyamula paphewa ndi mitengo yonyamulira. Anatengakonso makangaza*+ ndi nkhuyu.
4 Nkhata yamaluwa yokongola imene maluwa ake akufota,+ yomwe ili pamwamba pa phiri m’chigwa chachonde, idzakhala ngati nkhuyu yoyambirira kucha+ chilimwe chisanafike, imene munthu akaiona amaithyola n’kuimeza msangamsanga.
7 Tsoka kwa ine,+ chifukwa ndakhala ngati munthu wanjala amene sanapeze zipatso kuti adye.+ Ndakhala ngati munthu amene sanapeze nkhuyu zoyambirira zimene anali kuzilakalaka, nthawi yokolola zipatso za m’chilimwe* ndi mphesa itatha.+