15 Ndi thupi lake,+ anathetsa chidani chimene chinalipo,+ chimene ndi Chilamulo chokhala ndi malamulo operekedwa monga malangizo.+ Anachithetsa kuti mogwirizana ndi iye, alenge munthu mmodzi watsopano+ kuchokera ku magulu awiri a anthu,+ ndi kukhazikitsa mtendere.