Aefeso 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 anatikhalitsa amoyo pamodzi ndi Khristu, ngakhale kuti tinali akufa m’machimo,+ (pakuti inu mwapulumutsidwa chifukwa cha kukoma mtima kwakukulu)+ Akolose 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndiponso, ngakhale kuti munali akufa m’machimo anu ndipo munali osadulidwa, Mulungu anakupatsani moyo kuti mukhale ogwirizana ndi Khristu,+ ndipo anatikhululukira machimo athu onse motikomera mtima.+
5 anatikhalitsa amoyo pamodzi ndi Khristu, ngakhale kuti tinali akufa m’machimo,+ (pakuti inu mwapulumutsidwa chifukwa cha kukoma mtima kwakukulu)+
13 Ndiponso, ngakhale kuti munali akufa m’machimo anu ndipo munali osadulidwa, Mulungu anakupatsani moyo kuti mukhale ogwirizana ndi Khristu,+ ndipo anatikhululukira machimo athu onse motikomera mtima.+