Genesis 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno Yehova anaonekera kwa Abulamu nʼkumuuza kuti: “Ndidzapereka dziko ili+ kwa mbadwa* zako.”+ Choncho Abulamu anamanga guwa lansembe pamalo amene Yehova anaonekera kwa iye. Genesis 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Zimenezi zitachitika, Yehova analankhula ndi Abulamu mʼmasomphenya kuti: “Usaope+ Abulamu. Ine ndine chishango chako.+ Mphoto yako idzakhala yaikulu kwambiri.”+ Genesis 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Abulamu anakhulupirira zimene Yehova anamuuza,+ ndipo Mulunguyo anamuona kuti ndi wolungama.+ Genesis 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Dzina lako silikhalanso Abulamu* koma likhala Abulahamu,* chifukwa ndidzakupangitsa kukhala tate wa mitundu yambiri. Yakobo 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Choncho lemba linakwaniritsidwa limene limati: “Abulahamu anakhulupirira zimene Yehova* anamuuza ndipo ankaonedwa kuti ndi wolungama,”+ choncho ankadziwika kuti ndi mnzake wa Yehova.*+
7 Ndiyeno Yehova anaonekera kwa Abulamu nʼkumuuza kuti: “Ndidzapereka dziko ili+ kwa mbadwa* zako.”+ Choncho Abulamu anamanga guwa lansembe pamalo amene Yehova anaonekera kwa iye.
15 Zimenezi zitachitika, Yehova analankhula ndi Abulamu mʼmasomphenya kuti: “Usaope+ Abulamu. Ine ndine chishango chako.+ Mphoto yako idzakhala yaikulu kwambiri.”+
5 Dzina lako silikhalanso Abulamu* koma likhala Abulahamu,* chifukwa ndidzakupangitsa kukhala tate wa mitundu yambiri.
23 Choncho lemba linakwaniritsidwa limene limati: “Abulahamu anakhulupirira zimene Yehova* anamuuza ndipo ankaonedwa kuti ndi wolungama,”+ choncho ankadziwika kuti ndi mnzake wa Yehova.*+