2 Mbiri 36:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho anawabweretsera mfumu ya Akasidi+ yomwe inapha anyamata awo ndi lupanga+ mʼnyumba yopatulika.+ Sinamvere chisoni mnyamata kapena namwali, wachikulire kapena wodwala.+ Mulungu anapereka zonse mʼmanja mwake.+ Yeremiya 34:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Pita ukauze Mfumu Zedekiya+ ya Yuda kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Ine ndikupereka mzindawu mʼmanja mwa mfumu ya Babulo ndipo idzauwotcha ndi moto.+ Ezekieli 24:1, 2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Yehova analankhulanso nane mʼchaka cha 9, mʼmwezi wa 10, pa tsiku la 10 la mweziwo, kuti: 2 “Iwe mwana wa munthu, lemba deti lalero,* ulembe tsiku lalero. Lero mfumu ya Babulo yayamba kuukira mzinda wa Yerusalemu.+
17 Choncho anawabweretsera mfumu ya Akasidi+ yomwe inapha anyamata awo ndi lupanga+ mʼnyumba yopatulika.+ Sinamvere chisoni mnyamata kapena namwali, wachikulire kapena wodwala.+ Mulungu anapereka zonse mʼmanja mwake.+
2 “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Pita ukauze Mfumu Zedekiya+ ya Yuda kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Ine ndikupereka mzindawu mʼmanja mwa mfumu ya Babulo ndipo idzauwotcha ndi moto.+
24 Yehova analankhulanso nane mʼchaka cha 9, mʼmwezi wa 10, pa tsiku la 10 la mweziwo, kuti: 2 “Iwe mwana wa munthu, lemba deti lalero,* ulembe tsiku lalero. Lero mfumu ya Babulo yayamba kuukira mzinda wa Yerusalemu.+