Salimo 118:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mwala umene omanga nyumba anaukanaWakhala mwala wapakona* wofunika kwambiri.+ Yesaya 42:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Taonani mtumiki wanga+ amene ndikumuthandiza, Wosankhidwa wanga+ amene amandisangalatsa,+ Ine ndaika mzimu wanga mwa iye.+Iye adzabweretsa chilungamo kwa anthu a mitundu ina.+ Mateyu 21:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Ndiyeno Yesu anawauza kuti: “Paja Malemba amanena kuti, ‘Mwala umene omanga nyumba anaukana wakhala mwala wapakona wofunika kwambiri.*+ Umenewu wachokera kwa Yehova* ndipo ndi wodabwitsa mʼmaso mwathu.+ Kodi simunawerenge zimeneziʼ? Machitidwe 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yesu ameneyu ndi ‘mwala umene inu omanga nyumba munauona ngati wopanda pake, umene tsopano wakhala mwala wofunika kwambiri wapakona.’+
42 Taonani mtumiki wanga+ amene ndikumuthandiza, Wosankhidwa wanga+ amene amandisangalatsa,+ Ine ndaika mzimu wanga mwa iye.+Iye adzabweretsa chilungamo kwa anthu a mitundu ina.+
42 Ndiyeno Yesu anawauza kuti: “Paja Malemba amanena kuti, ‘Mwala umene omanga nyumba anaukana wakhala mwala wapakona wofunika kwambiri.*+ Umenewu wachokera kwa Yehova* ndipo ndi wodabwitsa mʼmaso mwathu.+ Kodi simunawerenge zimeneziʼ?
11 Yesu ameneyu ndi ‘mwala umene inu omanga nyumba munauona ngati wopanda pake, umene tsopano wakhala mwala wofunika kwambiri wapakona.’+