Genesis 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ufumu wake unayambira ku Babele,+ Ereke,+ Akadi mpaka ku Kaline m’dziko la Sinara.+ Genesis 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mzindawo unatchedwa Babele,+ chifukwa kumeneko, Yehova anasokoneza chilankhulo cha anthu onse, ndipo Yehova anabalalitsira+ anthuwo padziko lonse lapansi.
9 Mzindawo unatchedwa Babele,+ chifukwa kumeneko, Yehova anasokoneza chilankhulo cha anthu onse, ndipo Yehova anabalalitsira+ anthuwo padziko lonse lapansi.