Aefeso 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndiponso kuti kudzera mwa mtengo wozunzikirapo*+ ayanjanitse+ magulu awiri a anthuwo kwa Mulungu, ndipo anthuwo akhale thupi limodzi,+ chifukwa anali atapheratu chidanicho+ kudzera mwa iye mwini.
16 Ndiponso kuti kudzera mwa mtengo wozunzikirapo*+ ayanjanitse+ magulu awiri a anthuwo kwa Mulungu, ndipo anthuwo akhale thupi limodzi,+ chifukwa anali atapheratu chidanicho+ kudzera mwa iye mwini.